Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 48:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti iwo amadzitcha kuti amakhala mumzinda woyera,+ ndipo amadalira Mulungu wa Isiraeli+ amene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+

  • Yeremiya 44:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Tsopano imvani mawu a Yehova, inu nonse a ku Yuda amene mukukhala mu Iguputo muno.+ Yehova wanena kuti: “Ine ndalumbira m’dzina langa+ kuti m’dziko lonse la Iguputo simudzapezeka munthu aliyense wa ku Yuda woitanira pa dzina langa+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Ambuye Wamkulu Koposa!’+

  • Yeremiya 48:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Mowabu wafunkhidwa, ndipo munthu wina adzaukira mizinda yake.+ Anyamata osankhidwa a m’mizindayo apita kokaphedwa,’+ yatero Mfumu imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+

  • Malaki 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Aliyense wochita zachinyengo popereka nsembe nyama yachilema ndi wotembereredwa. Iye amalonjeza ndi kupereka nsembe nyama yachilema kwa Yehova pamene nyama yamphongo yabwinobwino, ali nayo pagulu la ziweto zake.+ Ine ndine Mfumu yaikulu+ ndipo dzina langa lidzaopedwa pakati pa anthu a mitundu ina,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena