Yesaya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+ Yeremiya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena.
14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+
8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena.