-
Yeremiya 44:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Choncho imvani mawu a Yehova, inu nonse a ku Yuda amene mukukhala mʼdziko la Iguputo. Yehova wanena kuti: “Ine ndikulumbira pa dzina langa lalikulu kuti mʼdziko lonse la Iguputo simudzapezeka munthu aliyense wa ku Yuda+ wolumbira mʼdzina langa kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Ambuye Wamkulu Koposa!’+
-