Oweruza 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mika anati: “Tsopano ndadziwa kuti Yehova andichitira zabwino, chifukwa Mlevi wakhala wansembe wanga.”+ Yeremiya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+ Aroma 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ngati ndiwe Myuda dzina lokha+ ndipo umadalira chilamulo+ ndi kunyadira Mulungu,+
13 Choncho Mika anati: “Tsopano ndadziwa kuti Yehova andichitira zabwino, chifukwa Mlevi wakhala wansembe wanga.”+
2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+