Yesaya 45:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mbewu+ yonse ya Isiraeli idzaona kuti inalondola+ potumikira Yehova ndipo idzadzitama.’”+ Yohane 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”
41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”