Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+

      Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+

      Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+

      Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+

  • Yesaya 63:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+

  • Yesaya 64:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+

  • Malaki 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Mwana amalemekeza bambo ake+ ndipo wantchito amalemekeza mbuye wake.+ Ngati ine ndili atate,+ ulemu wanga uli kuti?+ Ngati ndili Ambuye Wamkulu, n’chifukwa chiyani simundiopa?’+ watero Yehova wa makamu kwa inu ansembe amene mukunyoza dzina langa.+

      “‘Inu mukunena kuti: “Kodi dzina lanu talinyoza motani?”’

  • Malaki 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena