Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale? Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 17
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale?