Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+
2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+