13 Unali kuvala zinthu zagolide ndi zasiliva ndiponso nsalu zabwino kwambiri. Unali kuvala nsalu zamtengo wapatali ndi chovala cha nsalu yopeta.+ Unkadya ufa wosalala, uchi, ndi mafuta+ ndipo unakhala chiphadzuwa. Patapita nthawi unakhala woyenera ufumu.’”+