Yeremiya 46:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ yatero Mfumu, imene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,‘Iye* adzabwera nʼkuonekera ngati phiri la Tabori+ pakati pa mapiri enaNdiponso ngati phiri la Karimeli+ mʼmphepete mwa nyanja.
18 ‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ yatero Mfumu, imene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,‘Iye* adzabwera nʼkuonekera ngati phiri la Tabori+ pakati pa mapiri enaNdiponso ngati phiri la Karimeli+ mʼmphepete mwa nyanja.