Yoswa 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maere a 4+ anagwera Isakara,+ kapena kuti ana a Isakara motsatira mabanja awo. Yoswa 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake. Oweruza 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Debora anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 a fuko la Nafitali ndi la Zebuloni ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori. Salimo 89:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munapanga kumpoto ndi kumʼmwera.Mapiri a Tabori+ ndi Herimoni+ amatamanda dzina lanu mosangalala.
22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.
6 Debora anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 a fuko la Nafitali ndi la Zebuloni ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori.