Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.

  • Deuteronomo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Usavutitse Amowabu kapena kuchita nawo nkhondo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko lawo kuti likhale lako. Ndinapereka Ari+ kwa ana a Loti kuti akhale malo awo.+

  • Oweruza 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 ndipo anaiuza kuti:

      “Yefita wanena kuti, ‘Aisiraeli sanatenge dziko la Mowabu+ ndi dziko la ana a Amoni.+

  • 2 Mbiri 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano taonani zimene akuchita ana a Amoni,+ ana a Mowabu+ ndi a kudera lamapiri la Seiri.+ Inu simunalole kuti Aisiraeli alowe m’dziko lawo pamene anali kutuluka m’dziko la Iguputo ndipo anawasiya osawawononga.+

  • Machitidwe 17:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena