2 Samueli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inapatula siliva ndi golide wochokera ku Siriya, Mowabu,+ kwa ana a Amoni, Afilisiti,+ Aamaleki+ ndiponso siliva ndi golide amene anafunkha kwa Hadadezeri mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba.+
12 Inapatula siliva ndi golide wochokera ku Siriya, Mowabu,+ kwa ana a Amoni, Afilisiti,+ Aamaleki+ ndiponso siliva ndi golide amene anafunkha kwa Hadadezeri mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba.+