2 Samueli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa,+ ndipo anawalanda mzinda wa Metege-ama.