2 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+ 1 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.
18 Anandilanditsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Anandilanditsa kwa odana nane chifukwa anali amphamvu kuposa ine.+
18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.