Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko limene latsala ndi ili:+ Madera onse a Afilisiti+ ndi madera onse a Agesuri.+ 2 Samueli 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa.
15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa.