Ekisodo 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Dziko limene ndidzakupatsa lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita izi, chifukwa anthu okhala m’dzikomo ndidzawapereka m’manja mwako, ndipo iwe udzawathamangitsa pamaso pako.+ Zefaniya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+
31 “Dziko limene ndidzakupatsa lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita izi, chifukwa anthu okhala m’dzikomo ndidzawapereka m’manja mwako, ndipo iwe udzawathamangitsa pamaso pako.+
5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+