2 Samueli 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide. Davide atamva zimenezi, anakabisala kumalo ovuta kufikako.+ 2 Samueli 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi, Afilisiti aja anabweranso+ ndi kuyamba kuyendayenda m’chigwa cha Arefai.+
17 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide. Davide atamva zimenezi, anakabisala kumalo ovuta kufikako.+