1 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira. 1 Samueli 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti. 1 Samueli 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+ 2 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo n’kuti Davide ali m’malo ovuta kufikako,+ ndiponso n’kuti mudzi wa asilikali+ a Afilisiti uli ku Betelehemu.
22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira.
5 Patapita nthawi, Gadi+ mneneri anauza Davide kuti: “Usakhalenso m’malo ovuta kufikako. Uchokeko ndi kubwera m’dziko la Yuda.”+ Choncho Davide anachokako ndi kulowa munkhalango ya Hereti.
22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+
14 Pamenepo n’kuti Davide ali m’malo ovuta kufikako,+ ndiponso n’kuti mudzi wa asilikali+ a Afilisiti uli ku Betelehemu.