1 Samueli 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Davide anachoka kumeneko ndi kukakhala m’malo ovuta kufikako a ku Eni-gedi.+ Miyambo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+