Salimo 57:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Kwa wotsogolera nyimbo. “Musandiwononge.” Salimo la Davide. Mikitamu.* Pa nthawi imene anathawa Sauli n’kukalowa m’phanga.+ Salimo 142:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Masikili.* Salimo ndiponso pemphero la Davide, pamene anali kukhala kuphanga.+ Aheberi 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.
Kwa wotsogolera nyimbo. “Musandiwononge.” Salimo la Davide. Mikitamu.* Pa nthawi imene anathawa Sauli n’kukalowa m’phanga.+
38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.