1 Mafumu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+ 1 Mafumu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atafika kumeneko, analowa m’phanga+ kuti usiku agone mmenemo. Kenako anamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Ukufuna chiyani kuno Eliya?”+
4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+
9 Atafika kumeneko, analowa m’phanga+ kuti usiku agone mmenemo. Kenako anamva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Ukufuna chiyani kuno Eliya?”+