1 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ nʼkuthawira kuphanga la Adulamu.+ Azichimwene ake ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ake atamva zimenezi, ananyamuka nʼkumutsatira.
22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ nʼkuthawira kuphanga la Adulamu.+ Azichimwene ake ndi anthu onse amʼnyumba ya bambo ake atamva zimenezi, ananyamuka nʼkumutsatira.