1 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira.
22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira.