13 Ndiyeno pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu.+ Apa n’kuti Afilisiti atamanga msasa wa mahema m’chigwa cha Arefai.+
15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi gulu lankhondo la Afilisiti linali litamanga msasa m’chigwa cha Arefai.+