1 Mbiri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi gulu lankhondo la Afilisiti linali litamanga msasa m’chigwa cha Arefai.+
15 Kenako, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuthanthwe, kuphanga la Adulamu.+ Pa nthawiyi gulu lankhondo la Afilisiti linali litamanga msasa m’chigwa cha Arefai.+