2 Samueli 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu.+ Apa n’kuti Afilisiti atamanga msasa wa mahema m’chigwa cha Arefai.+
13 Ndiyeno pa nthawi yokolola, atatu mwa atsogoleri 30+ anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu.+ Apa n’kuti Afilisiti atamanga msasa wa mahema m’chigwa cha Arefai.+