Yoswa 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yarimuti,+ Adulamu,+ Soko,+ Azeka,+ 1 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira. Mika 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwe mkazi wokhala ku Maresha+ ndidzakubweretsera wolanda zinthu za ena.+ Ulemerero wa Isiraeli udzafika ku Adulamu.+
22 Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira.
15 Iwe mkazi wokhala ku Maresha+ ndidzakubweretsera wolanda zinthu za ena.+ Ulemerero wa Isiraeli udzafika ku Adulamu.+