1 Samueli 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero iye anawasiya m’manja mwa mfumu ya Mowabu, moti iwo anapitiriza kukhala kumeneko masiku onse amene Davide anakhala m’malo ovuta kufikako.+ 1 Mbiri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amuna ena a fuko la Benjamini ndi la Yuda anayenda mpaka kukafika kwa Davide, kumalo ovuta kufikako.+
4 Chotero iye anawasiya m’manja mwa mfumu ya Mowabu, moti iwo anapitiriza kukhala kumeneko masiku onse amene Davide anakhala m’malo ovuta kufikako.+
16 Amuna ena a fuko la Benjamini ndi la Yuda anayenda mpaka kukafika kwa Davide, kumalo ovuta kufikako.+