Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero iye anawasiya m’manja mwa mfumu ya Mowabu, moti iwo anapitiriza kukhala kumeneko masiku onse amene Davide anakhala m’malo ovuta kufikako.+

  • 1 Samueli 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano Davide anayamba kukhala m’chipululu, m’malo ovuta kufikako. Iye anapitiriza kukhala m’dera lamapiri m’chipululu cha Zifi,+ ndipo Sauli anali kumufunafuna nthawi zonse,+ koma Mulungu sanam’pereke m’manja mwake.+

  • 1 Samueli 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zitatero, Davide analumbirira Sauli. Kenako Sauliyo anapita kwawo,+ koma Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kumalo ovuta kufikako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena