Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Apanso Sauli anachita mantha kwambiri ndi Davide, moti anali kudana ndi Davide nthawi zonse.+

  • 1 Samueli 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+

  • 1 Samueli 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Davide anati mumtima mwake: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Palibe chimene ndingachite choposa kuthawira+ kudziko la Afilisiti.+ Ndiyeno Sauli adzagwa ulesi ndipo adzasiya kundifunafuna m’dziko lonse la Isiraeli.+ Pamenepo ndidzakhala nditapulumuka m’manja mwake.”

  • Salimo 54:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,

      Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+

      Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena