Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+ Salimo 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+ Salimo 86:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+
16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+
3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+
14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+