Salimo 59:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Madzulo amabweranso.+Ndipo amauwa ngati agalu+ ndi kuzungulira mzinda wonse.+ Luka 22:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Tsopano amuna amene anagwira Yesu aja anayamba kumuchitira zachipongwe,+ ndi kumumenya.+ Afilipi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chenjerani ndi agalu.+ Chenjerani ndi ochita ntchito zovulaza. Chenjerani ndi anthu amene amachita mdulidwe.+ Chivumbulutso 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu,+ amene amachita zamizimu,+ adama,+ opha anthu, opembedza mafano, ndi aliyense wokonda kulankhula ndi kuchita zachinyengo.’+
2 Chenjerani ndi agalu.+ Chenjerani ndi ochita ntchito zovulaza. Chenjerani ndi anthu amene amachita mdulidwe.+
15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu,+ amene amachita zamizimu,+ adama,+ opha anthu, opembedza mafano, ndi aliyense wokonda kulankhula ndi kuchita zachinyengo.’+