Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani anga andizungulira ngati agalu.+Andizungulira ngati gulu la anthu ochita zoipa,+Mofanana ndi mkango, iwo akundiluma manja ndi mapazi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,8/2012, tsa. 19 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 14
16 Adani anga andizungulira ngati agalu.+Andizungulira ngati gulu la anthu ochita zoipa,+Mofanana ndi mkango, iwo akundiluma manja ndi mapazi.+