2 Samueli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Abisalomu anafunsa Ahitofeli kuti: “Amuna inu, nenani maganizo anu.+ Tichite chiyani?” Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.