Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+ Yesaya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+ Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+
10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+
27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+