Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+

      Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+

      Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+

  • Maliko 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+

  • Yohane 11:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho,+ anati: “Palibe chimene mukudziwa inu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena