1 Samueli 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Sauli anaponya mkondo uja+ ndi kunena kuti: “Ndilasa Davide ndi kumukhomerera kukhoma* ndi mkondowu!”+ Koma Davide anamuthawa, ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.+ 1 Samueli 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+ Yohane 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+
11 Ndiyeno Sauli anaponya mkondo uja+ ndi kunena kuti: “Ndilasa Davide ndi kumukhomerera kukhoma* ndi mkondowu!”+ Koma Davide anamuthawa, ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.+
10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+
13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+