1 Samueli 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Sauli anaponya mkondo uja+ ndi kunena kuti: “Ndilasa Davide ndi kumukhomerera kukhoma* ndi mkondowu!”+ Koma Davide anamuthawa, ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.+ 1 Samueli 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli anamvera mawu a Yonatani, ndipo analumbira kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Davide saphedwa.” Salimo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzawononga olankhula bodza.+Munthu wokhetsa magazi+ ndi wachinyengo,+ Yehova amaipidwa naye. Mlaliki 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+
11 Ndiyeno Sauli anaponya mkondo uja+ ndi kunena kuti: “Ndilasa Davide ndi kumukhomerera kukhoma* ndi mkondowu!”+ Koma Davide anamuthawa, ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.+
6 Sauli anamvera mawu a Yonatani, ndipo analumbira kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Davide saphedwa.”
13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+