Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ 1 Samueli 14:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo, Mlanditsi wa Isiraeli, munthu amene wachititsa tchimoli ayenera kufa ndithu,+ ngakhale atakhala Yonatani mwana wanga.” Koma panalibe ngakhale munthu mmodzi womuyankha mwa anthu onsewo. Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+
39 Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo, Mlanditsi wa Isiraeli, munthu amene wachititsa tchimoli ayenera kufa ndithu,+ ngakhale atakhala Yonatani mwana wanga.” Koma panalibe ngakhale munthu mmodzi womuyankha mwa anthu onsewo.
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+