Mlaliki 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Usamapupulume kulankhula, ndipo mtima wako+ usamafulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba+ koma iwe uli padziko lapansi. N’chifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+
2 Usamapupulume kulankhula, ndipo mtima wako+ usamafulumire kulankhula pamaso pa Mulungu woona,+ chifukwa Mulungu woona ali kumwamba+ koma iwe uli padziko lapansi. N’chifukwa chake suyenera kulankhula zambiri.+