Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Mlaliki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yong’amba+ ndi nthawi yosoka.+ Nthawi yokhala chete+ ndi nthawi yolankhula.+ Mateyu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwe popemphera, usanene zinthu mobwerezabwereza+ ngati mmene amachitira anthu a mitundu ina, chifukwa iwo amaganiza kuti Mulungu awamvera akanena mawu ambirimbiri.
19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
7 Iwe popemphera, usanene zinthu mobwerezabwereza+ ngati mmene amachitira anthu a mitundu ina, chifukwa iwo amaganiza kuti Mulungu awamvera akanena mawu ambirimbiri.