Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero Yonatani analankhula zabwino+ za Davide kwa Sauli bambo ake, kuti: “Mfumu isachimwire+ mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakuchimwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.+

  • 1 Samueli 25:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako anagwada pamapazi+ a Davide ndi kunena kuti: “Zolakwa zonse zikhale pa ine+ mbuyanga. Chonde, lolani kapolo wanu wamkazi alankhule nanu+ ndipo mvetserani mawu a kapolo wanu.

  • Esitere 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti ngati iwe ukhala chete pa nthawi ino, thandizo ndi chipulumutso cha Ayuda zidzachokera kwina.+ Koma anthu inu, iwe ndi nyumba ya bambo ako, nonse mudzatheratu. Ndipo ndani akudziwa? Mwina iwe wakhala mfumukazi kuti uthandize pa nthawi ngati imeneyi.”+

  • Salimo 145:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo adzanena za ulemerero wa ufumu wanu.+

      Ndi kulankhula za mphamvu zanu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena