1 Samueli 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma Yonatani anayankha Sauli bambo ake kuti: “Aphedwe chifukwa chiyani?+ Walakwanji?”+ 1 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+ Miyambo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+
14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+
9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+