1 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli. 1 Samueli 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero Sauli anachotsa Davide kuti asamakhale naye pafupi,+ ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide anali kutsogolera asilikali amenewo.+
5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli.
13 Chotero Sauli anachotsa Davide kuti asamakhale naye pafupi,+ ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide anali kutsogolera asilikali amenewo.+