Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Iwe khala wolimba mtima kwambiri ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Uonetsetse kuti ukutsatira malamulo onse amene mtumiki wanga Mose anakulamula.+ Malamulowo usawasiye ndi kupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ kuti uchite mwanzeru kulikonse kumene udzapitako.+

  • 1 Samueli 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno akalonga+ a Afilisiti akatuluka kudzamenya nkhondo, Davide anali kuchita zinthu mwanzeru kwambiri+ mwa atumiki onse a Sauli, moti dzina la Davide linatchuka kwambiri.+

  • Miyambo 14:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena