1 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli.
5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli.