2 Samueli 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri. 2 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.
31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri.
19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.