Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ 2 Mafumu 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu Hezekiya+ itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake+ n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
19 Mfumu Hezekiya+ itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake+ n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+