Yesaya 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mfumu Hezekiya itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+
37 Mfumu Hezekiya itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+